Kuchokera ku vumbulutso limeneri bukhu iri linabwera., “Mpingo Waukulu” lolembedwa ndi Bishop Dag Heward-Mills, m’busa wa umodzi mwa mipingo yaikulu kwambiri ku Ghana. Mpingo wanu ndi utumiki wanu sudzakhalanso chimodzi modzi mukawerenga bukhu lolimbikitsali!“Dr. Heward-Mills ndi wodzipereka kwa Ambuye Yesu Khristu ndi ntchito yotenga mbali pa kulalikira ku dziko lonse. Ndi mtsogoleri wamphamvu ndinso chitsanzo ku mautumiki onse, ndipo ife ku “Church Growth International”, ndife olemekezedwa kudziwa ndikumutcha Dr. Dag Heward-Mills mnzathu komanso wogwira naye limodzi ntchito mu kholola lalikulu mu minda ya padziko.”
-Dr. Yonggi Cho
Wamkulu, Church Growth International